Maphunziro a chidule a Baibulo kwa a Khristu a tsopano komanso amene akukula kumene
MALONJE KWA OPHUNZIRA Tsopano ndinu Mkhristu. Mukufunika kuphunzira kukula ngati Mkhristu. Muphunzira maphunziro asanu ndi atatu a kukula ngati Mkhristu. Phunzirani phunziro lililonse pa nokha...